Miyambi 26:26-28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

26. Angakhale abisa udani wace pocenjera,Koma udio wace udzabvumbulutsidwa posonkhana anthu.

27. Wokumba dzenje adzagwamo,Wogubuduza mwala, udzabweranso pa iye mwini.

28. Lilime lonama lida omwewo linawasautsa;Ndipo m'kamwa mosyasyalika mungoononga.

Miyambi 26