Miyambi 25:8-10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Usaturuke mwansontho kukalimbana,Ungalephere pa kutha kwace,Atakucititsa mnzako manyazi.

9. Nena mlandu wako ndi mnzako,Osaulula zinsinsi za mwini;

10. Kuti wakumva angakutonze,Mbiri yako yoipa ndi kusacoka.

Miyambi 25