Miyambi 23:21-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Pakuti wakumwaimwa ndi wosusukayo adzasauka;Ndipo kusinza kudzabveka munthu nsanza.

22. Tamvera atate wako anakubala,Usapeputse amako atakalamba.

23. Gula ntheradi, osaigulitsa;Nzeru, ndi mwambo, ndi luntha.

Miyambi 23