Miyambi 21:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mtima wa mfumu uli m'dzanja la Yehova ngati mitsinje ya madzi;Aulozetsa komwe afuna.

2. Njira zonse za munthu zilungama pamaso pace;Koma Yehova ayesa mitima.

Miyambi 21