Miyambi 19:7-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

7. Abale onse a wosauka amuda;Nanga mabwenzi ace kodi satanimphirana naye?Awatsata ndi mau, koma kuli zi.

8. Wolandira nzeru akonda moyo wace;Wosunga luntha adzapeza zabwino.

9. Mboni yonama sidzapulumuka cilango;Wolankhula mabodza adzaonongeka.

Miyambi 19