Miyambi 19:4-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

4. Cuma cionjezetsa mabwenzi ambiri;Koma mnzace wa waumphawi amleka.

5. Mboni yonama sidzakhala yosalangidwa;Wolankhula mabodza sadzapulumuka.

6. Ambiri adzapembedza waufulu;Ndipo yense ndi bwenzi la munthu wopatsa.

Miyambi 19