Miyambi 18:23-24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. Wosauka amadandaulira;Koma wolemera ayankha mwaukali.

24. Woyanjana ndi ambiri angodziononga;Koma liripo bwenzi lipambana ndi mbale kuumirira.

Miyambi 18