Miyambi 13:23-25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

23. M'kulima kwa osauka muli zakudya zambiri;Koma zinazo zimaonongeka posowa ciweruzo.

24. Wolekereramwanace osammenya amuda;Koma womkonda amyambize kumlanga.

25. Wolungama adya nakhutitsa moyo wace;Koma mimba ya oipa idzasowa.

Miyambi 13