Miyambi 12:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Cinyengo ciri m'mitima ya oganizira zoipa;Koma aphungu a mtendere amakondwa.

21. Palibe bvuto lidzagwera wolungama;Koma amphulupulu adzadzazidwa ndi zoipa,

22. Milomo yonama inyansa Yehova;Koma ocita ntheradi amsekeretsa.

Miyambi 12