Miyambi 10:31-32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

31. M'kamwa mwa wolungama mulankhula nzeru;Koma lilime lokhota lidzadulidwa.

32. Milomo ya wolungama idziwa zokondweretsa;Koma m'kamwa mwa oipa munena zokhota,

Miyambi 10