Miyambi 10:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mwana wanzeru akondweretsa atate;Koma mwana wopusa amvetsa amace cisoni.

2. Cuma ca ucimo sicithangata:Koma cilungamo cipulumutsa kuimfa.

Miyambi 10