Mateyu 9:37-38 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

37. Pomwepo ananena kwa ophunzira ace, Zotuta zicurukadi koma anchito ali owerengeka.

38. Cifukwa cace pempherani Mwini zotuta kuti akokose anchito kukututakwace.

Mateyu 9