Mateyu 26:65-68 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

65. Pomwepo mkuru wa ansembe 6 anang'amba zobvala zace, nati, Acitira Mulungu mwano; tifuniranji mboni zina? onani, tsopano mwamva mwanowo;

66. muganiza bwanji? lwo anayankha nati, 7 Ali woyenera kumupha,

67. 8 Pomwepo iwo anathira malobvu pankhope pace, nambwanyula Iye; ndipo ena anampanda kofu,

68. nati, 9 Utilote ife, Kristu Iwe; wakumenya Iwe ndani?

Mateyu 26