Mateyu 23:38-39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

38. Onani, nyumba yanu yasiyidwa kwa inu yabwinja.

39. Pakuti ndinena kwa inu, Simudzandionanso Ine, kuyambira tsopano, kufikira mudzanena,Wolemekezedwa Iye amene akudza m'dzina la Ambuye.

Mateyu 23