Yesu ananena kwa iwo, 1 Kodi simunawerenga konse m'malembo,Mwala umene anaukana omanga nyumbaWomwewu unakhala mutu wa pangondya:ici cinacokera kwa Ambuye,Ndipo ciri cozizwitsa m'maso mwathu?