Mateyu 21:3-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Ndipo munthu akanena kanthu ndi inu, mudzati, Ambuye asowa iwo, Ndipo pomwepo adzawatumiza.

4. Ndipo ici cinatero, kuti cikacitidwe conenedwa ndi mneneri kuti,

5. Tauzani mwanawamkazi wa Ziyoni,Taona, Mfumu yako idza kwa iwe,Wofatsa ndi wokwera pa buru,Ndi pa kaburu, mwana wa nyama yonyarnula katundu.

6. Ndipo ophunzirawo anamuka, nacita monga Yesu anawauza;

Mateyu 21