Mateyu 19:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onse amene adasiya nyumba, kapena abale, kapena alongo, kapena atate, kapena amai, kapena ana, kapena minda, cifukwa ca dzina langa, adzalandira zobwezeredwa zambirimbiri, nadzalowa moyo wosatha.

Mateyu 19

Mateyu 19:24-30