Mateyu 13:51-53 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

51. Mwamvetsa zonsezi kodi? lwo anati kwa Iye, inde.

52. Ndipo Iye anati kwa iwo, Cifukwa cace, mlembi ali yense, wophunzitsidwa mu Ufumu wa Kumwamba, ali wofanana ndi munthu mwini banja, amene aturutsa m'cuma cace zinthu zakale ndi zatsopano.

53. Ndipo panali, pamene Yesu anatha mafanizo awa, anacokera kumeneko.

Mateyu 13