Mateyu 12:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

kuti analowa m'nyumba ya Mulungu, nadya mikate yoonetsa, imene yosaloleka kudya iye kapena amene anali naye, koma ansembe okha okha.

Mateyu 12

Mateyu 12:1-9