Mateyu 10:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo musamaopa amene akupha thupi, koma moyo sangathe kuupha; koma makamaka muope Iye, wokhoza kuononga moyo ndi thupi lomwe m'gehena.

Mateyu 10

Mateyu 10:22-32