Masalmo 98:7-9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

7. Nyanja Ipfuule ndi kudzala kwace;Dziko lokhalamo anthu ndi iwo okhalamo;

8. Mitsinje iombe manja;Mapiri apfuule pamodzi mokondwera;

9. Pamaso pa Yehova, popeza akudza kudzaweruza dziko lapansi;Adzaweruza dziko lokhalamo anthu ndi cilungamo,Ndi mitundu ya anthu molunjika,

Masalmo 98