Masalmo 97:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova acita ufumu; dziko lapansi likondwere;Zisumbu zambiri zikondwerere.

2. Pomzinga pali mitambo ndi mdima;Cilungamo ndi ciweruzo ndizo zolimbitsa mpando wacifumu wace.

3. Moto umtsogolera,Nupsereza otsutsana naye pozungulirapo,

Masalmo 97