Masalmo 95:10-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

10. Zaka makumi anai mbadwo uwu unandimvetsa cisoni,Ndipo ndinati, Iwo ndiwo anthu osokerera mtima,Ndipo sadziwa njira zanga.

11. Cifukwa cace ndinalumbira mu mkwiyo wanga,Ngati adzalowa mpumulo wanga.

Masalmo 95