Masalmo 94:21-23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

21. Asonkhana pamodzi pa moyo wa wolungama,Namtsutsa wa mwazi wosacimwa.

22. Koma Yehova wakhala msanje wanga;Ndi Mulungu wanga thanthwe lothawirapo ine.

23. Ndipo anawabwezera zopanda pace zao,Nadzawaononga m'coipa cao;Yehova Mulungu wathu adzawaononga.

Masalmo 94