Masalmo 90:15-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

15. Tikondweretseni monga mwa masiku mudatizunzawa,Ndi zaka tidaona coipa.

16. Cocita Inu cioneke kwa atumiki anu,Ndi ulemerero wanu pa ana ao.

17. Ndipo cisomo cace ca Yehova Mulungu wathu cikhale pa ife;Ndipo mutikhazikitsire ife nchito ya manja athu;Inde, nchito ya manja athu muikhazikitse.

Masalmo 90