Masalmo 88:16-18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

16. Kuzaza kwanu kwandimiza;Zoopsa zanu zinandiononga,

17. Zinandizungulira ngati madzi tsiku lonse;Zinandizinga pamodzi.

18. Munandicotsera kutali wondikonda ndi bwenzi langa,Odziwana nane akhala kumdima.

Masalmo 88