Masalmo 88:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, Mulungu wa cipulumutso canga,Ndinapfuula pamaso panu usana ndi usiku,

2. Pemphero langa lidze pamaso panu;Mundicherere khutu kukuwa kwanga:

Masalmo 88