Masalmo 85:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Munacita zobvomereza dziko lanu, Yehova;Munabweza ukapolo wa Yakobo.

2. Munacotsa mphulupulu ya anthu anu,Munafotsera zolakwa zao zonse.

Masalmo 85