Masalmo 82:5-7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Sadziwa, ndipo sazindikira;Amayendayenda mumdima;Maziko onse a dziko lapansi agwedezeka.

6. Ndinati Ine, Inu ndinu milungu,Ndi ana a Wam'mwambamwamba nonsenu.

7. Komatu mudzafa monga anthu,Ndipo mudzagwa monga wina wa akulu.

Masalmo 82