Masalmo 78:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anakhazika mboni mwa Yakobo,Naika cilamulo mwa Israyeli,Ndizo analamulira atate athu,Akazidziwitse ana ao;

Masalmo 78

Masalmo 78:1-10