Masalmo 75:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti m'dzanja la Yehova muli cikho;Ndi vinyo wace acita thobvu;Cidzala ndi zosanganizira, ndipo atsanulako:Indedi, oipa onse a pa dziko lapansi adzamwaNadzagugudiza nsenga zace.

Masalmo 75

Masalmo 75:1-10