1. Fulumirani kundipulumutsa, Mulungu;Fulumirani kundithandiza, Yehova.
2. Acite manyazi, nadodomeAmene afuna moyo wanga:Abwezedwe m'mbuyo, napepulidwe.Amene akonda kundicitira coipa,
3. Abwerere, kukhale mphotho ya manyazi aoAmene akuti, Hede, hede.