Masalmo 68:34-35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

34. Bvomerezani kuti mphamvu nja Mulungu;Ukulu wace uli pa Israyeli,Ndi mphamvu yace m'mitambo.

35. Inu Mulungu, ndinu woopsa m'malo oyera anu;Mulungu wa Israyeli ndiye amene apatsa anthu ace mphamvu ndi cilimbiko.Alemekezeke Mulungu.

Masalmo 68