Masalmo 66:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pfuulirani kwa Mulungu, dziko lonse lapansi.

2. Yimbirani ulemerero wa dzina lace;Pomlemekeza mumcitire ulemerero.

3. Nenani kwa Mulungu, Ha, nchito zanu nzoopsa nanga!Cifukwa ca mphamvu yanu yaikuru adani anu adzagonjera Inu,

Masalmo 66