Masalmo 59:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ine, ndidzayimbira mphamvu yanu;Inde ndidzayimbitsa cifundo canu mamawa:Pakuti Inu mwakhala msanje wanga,Ndi pothawirapo ine tsiku la nsautso yanga.

Masalmo 59

Masalmo 59:8-17