Masalmo 56:12-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

12. Zowindira Inu Mulungu, ziri pa ine:Ndidzakucitirani zoyamika.

13. Pakuti mwalanditsa moyo wanga kuimfa:Simunatero nao mapazi anga kuti ndingagwe?Kuti ndiyende pamaso pa MulunguM'kuunika kwa amoyo.

Masalmo 56