Masalmo 55:8-11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

8. Ndikadafulumira ndipulumukeKu mphepo yolimba ndi namondwe.

9. Aonongeni, Ambuye, gawani lilime lao:Pakuti ndaona ciwawa ndi ndeu m'mudzimo.

10. Izizo ziuzungulira pa malinga ace usana ndi usiku;Ndipo m'kati mwace muli zapanda pace ndi cobvuta.

11. M'kati mwace muli kusakaza:Ciwawa ndi cinyengo sizicoka m'makwalala ace.

Masalmo 55