Masalmo 38:21-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Musanditaye, Yehova:Mulungu wanga, musakhale kutali ndi ine. Fulumirani kundithandiza,Ambuye, cipulumutso canga.