Masalmo 38:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova, musandidzudzule ndi mkwiyo wanu:Ndipo musandilange moopsa m'mtima mwanu.

2. Pakuti mibvi yanu yandilowa,Ndi dzanja lanu landigwera.

Masalmo 38