Masalmo 33:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Pfuulani mokondwera mwa Yehova, inu olungama mtima:Oongoka mtima ayenera kulemekeza.

2. Yamikani Yehova ndi zeze:Myimbireni ndi cisakasa ca zingwe khumi.

3. Mumyimbire Iye Nyimbo yatsopano;Muyimbe mwaluso kumveketsa mau.

Masalmo 33