Masalmo 26:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mundiweruze, Yehova, pakuti ndayenda m'ungwiro wanga:Ndipo ndakhulupirira Yehova, sindidzaterereka.

2. Mundiyesere, Yehova, ndipo mundisunthe;Yeretsani imso zanga ndi mtima wanga.

Masalmo 26