Masalmo 21:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Pakuti anakupangirani coipa:Anapangana ciwembu, osakhoza kucicita.

12. Pakuti mudzawabweza m'mbuyo,Popiringidza m'nsinga zanu pankhope pao,

13. Kwezekani, Yehova, mu mphamvu yanu:Potero tidzayimba ndi kulemekeza cilimbiko canu.

Masalmo 21