Masalmo 20:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Yehova akubvomereze tsiku la nsautso;Dzina la Mulungu wa Yakobo likuike pamsanje;

2. Likutumizire thandizo loturuka m'malo oyera,Ndipo likugwirizize kucokera m'Ziyoni;

3. Likumbukile zopereka zako zonse,Lilandire nsembe yako yopsereza;

Masalmo 20