Masalmo 2:9-12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

9. Udzawatyola ndi ndodo yacitsulo;Udzawaphwanya monga mbiya yawoumba.

10. Tsono, mafumu inu, citani mwanzeru:Langikani, oweruza inu a dziko lapansi.

11. Tumikirani Yehova ndi mantha,Ndipo kondwerani ndi cinthenthe.

12. Mpsompsoneni Mwanayo, kuti angakwiye, ndipo mungatayike m'njira,Ukayaka pang'ono pokha mkwiyo wace.Odala onse akumkhulupirira Iye.

Masalmo 2