Masalmo 18:27-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. Pakuti Inu muwapulumutsa anthu aumphawi;Koma maso okweza muwatsitsa.

28. Pakuti Inu muyatsa nyali yanga;Yehova, Mulungu wanga, aunikira mdima wanga.

29. Pakuti mwa Inu ndipyola khamu la anthu;Ndipo mwa Mulungu wanga ndilumphira linga.

Masalmo 18