Masalmo 150:3-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Mlemekezeni ndi kulira kwa lipenga;Mlemekezeni ndi cisakasa ndi zeze.

4. Mlemekezeni ndi lingaka ndi kuthira mang'ombe:Mlemekezeni ndi zoyimbira za zingwe ndi citoliro.

5. Mlemekezeni ndi nsanje zomveka:Mlemekezeni ndi nsanje zoliritsa.

6. Zonse zakupuma zilemekeze Yehova.Haleluya.

Masalmo 150