Masalmo 147:19-20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Aonetsa mau ace kwa Yakobo;Malemba ace, ndi maweruzo ace kwa Israyeli.

20. Sanatero nao anthu amtundu wina;Ndipo za maweruzo ace, sanawadziwa.Haleluya.

Masalmo 147