Masalmo 147:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Haleluya;Pakuti kuyimbira zomlemekeza Mulungu wathu nkokoma;Pakuti cikondwetsa ici, cilemekezo ciyenera.

2. Yehova amanga Yerusalemu;Asokolotsa otayika a Israyeli.

3. Aciritsa osweka mtima,Namanga mabala ao.

Masalmo 147