Masalmo 145:19-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Adzacita cokhumba iwo akumuopa;Nadzamva kupfuula kwao, nadzawapulumutsa.

20. Yehova asunga onse akukondana naye;Koma oipa onse adzawaononga.

21. Pakamwa panga padzanena cilemekezo ca Yehova;Ndi zinthu zonse zilemekeze dzina lace loyera ku nthawi za nthawi.

Masalmo 145