Masalmo 144:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kuti nkhokwe zathu zidzale, kutipatsa za mitundu mitundu;Ndi kuti nkhosa zathu ziswane zikwi zikwi, inde zikwi khumi kubusako.

Masalmo 144

Masalmo 144:9-15